Lied to this other born again hun kuti I am listening to Wendy’s music today ,huns is asking for my top 5 recent songs from her and I don’t even know any apart from ija ankafuna kugawa mbwanda kwa Lulu ija 😢
I remember in secondary school wina wake brought this movie kuti anthu aonele Ku video show but anthu ankafuna boys over flowers they ended up watching anthu ochepa after the show ended and wina snitched on them..
Munthu wina pa mowa ankafuna kundimenya ati 'how come at 27 you don't know where Beit-Bridge is? You mean pa Nyamapanda sumapadziwa?' To which I retorted that sindimapadziwadi chifukwa ndege simadutsa pa Beit-Bridge. You don't go to South Africa/Tanzania by bus. Kuvutika kumeneko